Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo Sauli anatenga amuna osankhidwa mwapadera 3,000+ mu Isiraeli monse, ndipo anapita kukafunafuna Davide+ ndi amuna amene anali kuyenda naye m’matanthwe amene mumakhala mbuzi za m’mapiri.+

  • Salimo 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye amabisalira anthu pafupi ndi midzi.

      Amabisalira munthu wosalakwa ndi kumupha.+

      ע [ʽAʹyin]

      Maso ake amafunafuna waumphawi.+

  • Salimo 37:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Woipa amalondalonda munthu wolungama,+

      Ndipo amafuna kuti amuphe.+

  • Mateyu 26:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha.

  • Machitidwe 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma chonde musalole kuti akunyengerereni, pakuti amuna oposa 40 akumudikirira panjira.+ Amenewa achita kulumbira modzitemberera kuti sadya kapena kumwa kanthu kufikira atamupha.+ Moti panopa akonzeka, akungoyembekezera chilolezo chanu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena