2 Samueli 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano mu Isiraeli yense munalibe mwamuna wina wotamandika kwambiri koposa Abisalomu chifukwa cha kukongola kwake.+ Iye analibe chilema chilichonse kuyambira kuphazi mpaka paliwombo. 2 Samueli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Yowabu anati: “Ndisachedwe chonchi ndi iwe!” Atatero anatenga mikondo itatu m’manja mwake ndi kulasa+ nayo mtima wa Abisalomu ali ndi moyo+ pakati pa mtengo waukulu.
25 Tsopano mu Isiraeli yense munalibe mwamuna wina wotamandika kwambiri koposa Abisalomu chifukwa cha kukongola kwake.+ Iye analibe chilema chilichonse kuyambira kuphazi mpaka paliwombo.
14 Pamenepo Yowabu anati: “Ndisachedwe chonchi ndi iwe!” Atatero anatenga mikondo itatu m’manja mwake ndi kulasa+ nayo mtima wa Abisalomu ali ndi moyo+ pakati pa mtengo waukulu.