1 Mafumu 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Alozetse mtima wathu+ kwa iye kuti tiyende m’njira zake zonse+ ndi kusunga malamulo ake,+ malangizo ake,+ ndi zigamulo zake,+ zimene analamula makolo athu. 2 Mbiri 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe, pali zinthu zabwino+ zimene zapezeka mwa inu, chifukwa mwachotsa mizati yopatulika m’dzikoli,+ ndipo mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+ Salimo 105:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Anachita zimenezi kuti asunge malangizo ake,+Ndi kusunga malamulo ake.+Tamandani Ya, anthu inu!+
58 Alozetse mtima wathu+ kwa iye kuti tiyende m’njira zake zonse+ ndi kusunga malamulo ake,+ malangizo ake,+ ndi zigamulo zake,+ zimene analamula makolo athu.
3 Komabe, pali zinthu zabwino+ zimene zapezeka mwa inu, chifukwa mwachotsa mizati yopatulika m’dzikoli,+ ndipo mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+