2 Samueli 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kwa munthu wokhalabe woyera, mudzadzisonyeza kuti ndinu woyera,+Kwa munthu wopotoka maganizo mudzachita zinthu ngati wopusa.+ Salimo 125:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma anthu obwerera kunjira zawo zokhotakhota,+Yehova adzawapereka ku chilango pamodzi ndi ochita zopweteka anzawo.+Ndipo mu Isiraeli mudzakhala mtendere.+
27 Kwa munthu wokhalabe woyera, mudzadzisonyeza kuti ndinu woyera,+Kwa munthu wopotoka maganizo mudzachita zinthu ngati wopusa.+
5 Koma anthu obwerera kunjira zawo zokhotakhota,+Yehova adzawapereka ku chilango pamodzi ndi ochita zopweteka anzawo.+Ndipo mu Isiraeli mudzakhala mtendere.+