1 Samueli 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero mwamunayo anaperekeza+ Davide ndi kupita kumene kunali achifwambawo, ndipo anawapeza atamwazikana m’dziko lonselo, akudya ndi kumwa, kuchita chiphwando+ chifukwa chakuti anafunkha zinthu zambiri m’dziko la Afilisiti ndi la Yuda.+ Yesaya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwachulukitsa mtundu,+ mwaupangitsa kusangalala kwambiri.+ Iwo asangalala pamaso panu ngati mmene amasangalalira pa nthawi yokolola,+ ngati anthu amene amasangalala akamagawana katundu amene alanda.+
16 Chotero mwamunayo anaperekeza+ Davide ndi kupita kumene kunali achifwambawo, ndipo anawapeza atamwazikana m’dziko lonselo, akudya ndi kumwa, kuchita chiphwando+ chifukwa chakuti anafunkha zinthu zambiri m’dziko la Afilisiti ndi la Yuda.+
3 Mwachulukitsa mtundu,+ mwaupangitsa kusangalala kwambiri.+ Iwo asangalala pamaso panu ngati mmene amasangalalira pa nthawi yokolola,+ ngati anthu amene amasangalala akamagawana katundu amene alanda.+