Salimo 119:104 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 104 Chifukwa cha malamulo anu ndimachita zinthu mozindikira.+N’chifukwa chake ndimadana ndi njira iliyonse yachinyengo.+ Miyambo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 mboni yachinyengo yonena mabodza,+ ndi aliyense woyambitsa mikangano pakati pa abale.+ Amosi 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+ Aroma 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chikondi+ chanu chisakhale cha chiphamaso.+ Nyansidwani ndi choipa,+ gwiritsitsani chabwino.+
104 Chifukwa cha malamulo anu ndimachita zinthu mozindikira.+N’chifukwa chake ndimadana ndi njira iliyonse yachinyengo.+
15 Danani ndi choipa ndipo muzikonda chabwino.+ Chitani zinthu zachilungamo pachipata cha mzinda,+ mwina Yehova Mulungu wa makamu adzakomera mtima+ otsala a Yosefe.’+