Ekisodo 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’dziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku anu.+ Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+
26 M’dziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku anu.+