Salimo 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wodala ndi munthu wamphamvu amene amakhulupirira Yehova,+Munthu amene sanacheukire anthu otsutsa,Kapena anthu amene anapatukira m’njira za mabodza.+ Salimo 127:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wodala ndi mwamuna wamphamvu amene wadzaza+ kachikwama kake ka mivi ndi mivi imeneyo.Abambo oterowo sadzachita manyazi,+Pakuti anawo adzalankhula ndi adani pachipata.
4 Wodala ndi munthu wamphamvu amene amakhulupirira Yehova,+Munthu amene sanacheukire anthu otsutsa,Kapena anthu amene anapatukira m’njira za mabodza.+
5 Wodala ndi mwamuna wamphamvu amene wadzaza+ kachikwama kake ka mivi ndi mivi imeneyo.Abambo oterowo sadzachita manyazi,+Pakuti anawo adzalankhula ndi adani pachipata.