Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo ndinayankha mfumuyo kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Kodi nkhope yanga ilekerenji kukhala yachisoni pamene mzinda+ umene makolo anga+ anaikidwako uli bwinja ndipo zipata zake zinatenthedwa ndi moto?”+

  • Salimo 84:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndimalakalaka mabwalo a Yehova ndipo ndafookeratu chifukwa cholakalaka mabwalowo.+

      Mtima wanga ndi thupi langa zikufuula mosangalala kwa Mulungu wamoyo.+

  • Salimo 102:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Atumiki anu akondwera ndi miyala ya mpanda wake,+

      Ndipo amakomera mtima fumbi lake.+

  • Yesaya 62:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Chifukwa cha Ziyoni sindidzakhala phee,+ ndipo chifukwa cha Yerusalemu+ sindidzakhala chete mpaka kulungama kwake kutakhala ngati kuwala,+ ndiponso mpaka chipulumutso chake chitakhala ngati muuni woyaka moto.+

  • Yeremiya 51:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 “Inu amene mwathawa lupanga, pitirizani kuthawa. Musaime chilili.+ Kumbukirani Yehova+ pamene muli kutali kwambiri ndipo mukumbukirenso Yerusalemu mumtima mwanu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena