Salimo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 107:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo,+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+
13 Iwo anayamba kuitana Yehova kuti awathandize m’masautso awo,+Ndipo iye anawapulumutsa ku mavuto awo monga mwa nthawi zonse.+