Yesaya 49:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndimvereni zilumba inu,+ ndipo mvetserani, inu mitundu ya anthu akutali.+ Yehova anandiitana+ ndili m’mimba.+ Ndili mkati mwa mayi anga, anatchula dzina langa.+ Luka 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Choncho anafuula ndi mawu amphamvu, kuti: “Ndiwe wodalitsidwa mwa akazi onse. N’chodalitsidwanso+ chipatso cha mimba yako! Agalatiya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma pamene Mulungu, amene anandichititsa kuti ndibadwe, anandiitana+ mwa kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kunamukomera
49 Ndimvereni zilumba inu,+ ndipo mvetserani, inu mitundu ya anthu akutali.+ Yehova anandiitana+ ndili m’mimba.+ Ndili mkati mwa mayi anga, anatchula dzina langa.+
42 Choncho anafuula ndi mawu amphamvu, kuti: “Ndiwe wodalitsidwa mwa akazi onse. N’chodalitsidwanso+ chipatso cha mimba yako!
15 Koma pamene Mulungu, amene anandichititsa kuti ndibadwe, anandiitana+ mwa kukoma mtima kwake kwakukulu,+ kunamukomera