Salimo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikaitana, mundiyankhe inu Mulungu wanga wolungama.+M’masautso anga mundiimiritse pamalo otakasuka.Mundikomere mtima+ ndipo imvani pemphero langa. Salimo 130:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga Yehova.+Makutu anu amve mawu anga ochonderera.+
4 Ndikaitana, mundiyankhe inu Mulungu wanga wolungama.+M’masautso anga mundiimiritse pamalo otakasuka.Mundikomere mtima+ ndipo imvani pemphero langa.