Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti ndinamva zoipa zimene ambiri anali kunena.+ Zinali zochititsa mantha paliponse. Iwo anali kunena kuti, “Fotokozani kuti ifenso tinene za iye.”+ Munthu aliyense anali kundiuza kuti “Mtendere!” koma anali kundiyang’anira kuti ndilakwitse chinachake+ ndipo anali kunena kuti: “Achita chinachake chopusa+ ameneyu ndipo timugonjetsa ndi kumubwezera.”

  • Luka 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena