Yobu 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akunyansidwa nane, ndipo akukhala patali ndi ine.+Sakuzengereza kundilavulira kumaso.+ Miyambo 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wosauka amadedwa ngakhale ndi mnzake,+ koma munthu wolemera amakhala ndi anzake ambiri.+ Yakobo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma inu simulemekeza munthu wosauka. Kodi si olemera amene amakusautsani+ ndi kukukokerani kumabwalo amilandu?+
6 Koma inu simulemekeza munthu wosauka. Kodi si olemera amene amakusautsani+ ndi kukukokerani kumabwalo amilandu?+