Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 38:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+

      Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+

  • Salimo 88:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+

      Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+

      Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+

  • Mlaliki 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mumzindawo munali munthu wina wosauka koma wanzeru, amene anapulumutsa mzindawo chifukwa cha nzeru zake.+ Koma kenako palibe amene anakumbukira munthu wosaukayo.+

  • Yakobo 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 inu mumasangalala ndi wovala zapamwamba uja+ ndipo mumamuuza kuti: “Khalani pamalo pabwinopa,” koma kwa wosauka uja mumati: “Imirira choncho,” kapena: “Khala pansipa pafupi ndi chopondapo mapazi anga.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena