Yesaya 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akalonga ako ndi aliuma ndipo ndi anzawo a mbala.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu+ ndipo amafunafuna mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+ Ezekieli 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma bambo akewo, adzafa chifukwa cha zolakwa zawo,+ popeza anabera anthu mwachinyengo,+ anabera m’bale wawo zinthu mwauchifwamba+ ndipo anachita choipa chilichonse pakati pa anthu a mtundu wawo.+ Mika 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+
23 Akalonga ako ndi aliuma ndipo ndi anzawo a mbala.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu+ ndipo amafunafuna mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+
18 Koma bambo akewo, adzafa chifukwa cha zolakwa zawo,+ popeza anabera anthu mwachinyengo,+ anabera m’bale wawo zinthu mwauchifwamba+ ndipo anachita choipa chilichonse pakati pa anthu a mtundu wawo.+
11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+