Numeri 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Mose anapanga njoka yamkuwa+ ndi kuiika pamtengo wachizindikirowo.+ Ndipo zinachitikadi kuti munthu akalumidwa ndi njoka n’kuyang’ana+ njoka yamkuwayo, anali kukhalabe ndi moyo.+ Yeremiya 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Inetu ndikutumiza njoka pakati panu, njoka zapoizoni,+ zimene simungaziimbire nyimbo kuti muziseweretse,+ ndipo zidzakulumani ndithu,” watero Yehova.
9 Pamenepo Mose anapanga njoka yamkuwa+ ndi kuiika pamtengo wachizindikirowo.+ Ndipo zinachitikadi kuti munthu akalumidwa ndi njoka n’kuyang’ana+ njoka yamkuwayo, anali kukhalabe ndi moyo.+
17 “Inetu ndikutumiza njoka pakati panu, njoka zapoizoni,+ zimene simungaziimbire nyimbo kuti muziseweretse,+ ndipo zidzakulumani ndithu,” watero Yehova.