Salimo 140:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anola lilime lawo ndipo lakhala ngati la njoka.+M’milomo yawo muli poizoni wa mphiri.+ [Seʹlah.] Machitidwe 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anali kuyembekezera kuti atupa kapena agwa mwadzidzidzi n’kufa. Koma atayembekezera nthawi yaitali n’kuona kuti palibe choopsa chimene chikumuchitikira, anasintha maganizo awo ndi kuyamba kumunena kuti ndi mulungu.+
6 Iwo anali kuyembekezera kuti atupa kapena agwa mwadzidzidzi n’kufa. Koma atayembekezera nthawi yaitali n’kuona kuti palibe choopsa chimene chikumuchitikira, anasintha maganizo awo ndi kuyamba kumunena kuti ndi mulungu.+