Miyambo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kuti alandire malangizo+ amene amathandiza munthu kuzindikira,+ kuchita zolondola,+ zachilungamo+ ndi zowongoka.+ Miyambo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gwira malangizo,+ usawataye.+ Uwasunge bwino chifukwa iwo ndiwo moyo wako.+ Miyambo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wokonda malangizo* amakondanso kudziwa zinthu,+ koma wodana ndi chidzudzulo ndi wopanda nzeru.+
3 kuti alandire malangizo+ amene amathandiza munthu kuzindikira,+ kuchita zolondola,+ zachilungamo+ ndi zowongoka.+