Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Tsopano ngati inu mfumu mukuona kuti n’koyenera, uzani anthu afufuze+ m’nyumba ya chuma cha mfumu imene ili ku Babuloko, kuti aone ngati mfumu Koresi inaikadi lamulo+ loti nyumba ya Mulungu yomwe ili ku Yerusalemu imangidwenso. Inu mfumu mutitumizire chigamulo chanu pankhani imeneyi.”

  • Ezara 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Panali pa nthawi imeneyi pamene mfumu Dariyo inaika lamulo loti afufuze ndipo anafufuza m’nyumba yosungiramo mabuku ofotokoza mbiri yakale,+ momwe analinso kusungiramo zinthu zamtengo wapatali zimene zinaikidwa ku Babuloko.

  • Yobu 29:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndinali bambo weniweni kwa osauka,+

      Ndipo mlandu wa munthu amene sindinali kumudziwa ndinkaufufuza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena