Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano, bambo anga,+ onani. Taonani kansalu ka m’munsi mwa malaya anu akunja odula manja. Pakuti mmene ndinali kudula kansalu kameneka sindinakupheni. Ndiyetu dziwani ndi kuona kuti ndilibe maganizo oipa+ kapena oukira, ndipo sindinakuchimwireni, ngakhale kuti inuyo mukufunafuna moyo wanga kuti mundiphe.+

  • 1 Samueli 25:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Komabe, pali Yehova Mulungu wamoyo wa Isiraeli, amene wandigwira kuti ndisakuchitire choipa,+ ukanapanda kufulumira kudzakumana nane,+ ndithu sipakanatsala munthu wokodzera khoma+ m’banja la Nabala pofika mawa m’mawa.”

  • Aroma 12:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma “ngati mdani wako ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse chakumwa.+ Pakuti mwa kutero udzamuunjikira makala a moto pamutu pake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena