Miyambo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Woipa adzagwidwa ndi zolakwa zake zomwe,+ ndipo adzamangidwa m’zingwe za tchimo lake lomwe.+ 2 Timoteyo 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso kuti mwina nzeru zawo zingabwereremo kuti awonjoke mumsampha+ wa Mdyerekezi, poona kuti wawagwira amoyo+ pofuna kukwaniritsa cholinga chake.
26 Komanso kuti mwina nzeru zawo zingabwereremo kuti awonjoke mumsampha+ wa Mdyerekezi, poona kuti wawagwira amoyo+ pofuna kukwaniritsa cholinga chake.