3 Koma Petulo anati: “Hananiya, n’chifukwa chiyani Satana+ wakulimbitsa mtima choncho kuti uyese kunamiza+ mzimu woyera+ ndi kubisa zina mwa ndalama za mtengo wa mundawo?
20 Ena mwa amenewa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda,+ ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa,* aphunzire kuti sayenera kulankhula zonyoza Mulungu.+