Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 15:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Kuopa Yehova ndi kumene kumaphunzitsa munthu kuchita zinthu mwanzeru,+ ndipo ulemerero umabwera pambuyo pa kudzichepetsa.+

  • Miyambo 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu asanagwe, mtima wake umadzikweza,+ ndipo asanapeze ulemerero, amadzichepetsa.+

  • Yesaya 57:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti Wapamwamba ndi Wokwezeka,+ yemwe adzakhalepo kwamuyaya+ ndiponso yemwe dzina lake ndi loyera,+ wanena kuti: “Ine ndimakhala kumwamba pamalo oyera.+ Ndimakhalanso ndi munthu wopsinjika ndi wa mtima wodzichepetsa,+ kuti nditsitsimutse mtima wa anthu onyozeka ndiponso kuti nditsitsimutse mtima wa anthu opsinjika.+

  • Mateyu 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chotero, aliyense amene adzadzichepetsa+ ngati mwana wamng’ono uyu ndi amene adzakhala wamkulu kwambiri mu ufumu wakumwamba.+

  • Afilipi 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena