Levitiko 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Usabere mnzako mwachinyengo+ ndipo usafwambe aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone m’nyumba mwako kufikira m’mawa.+ Deuteronomo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uzionetsetsa kuti wam’bwezera chikolecho dzuwa likangolowa,+ kuti akagone m’chovala chake.+ Pamenepo adzakudalitsa,+ ndipo udzakhala utachita chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wako.+
13 Usabere mnzako mwachinyengo+ ndipo usafwambe aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone m’nyumba mwako kufikira m’mawa.+
13 Uzionetsetsa kuti wam’bwezera chikolecho dzuwa likangolowa,+ kuti akagone m’chovala chake.+ Pamenepo adzakudalitsa,+ ndipo udzakhala utachita chilungamo pamaso pa Yehova Mulungu wako.+