Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha nzeru.+ Kudziwa Woyera Koposa, ndiko kumvetsa zinthu.+

  • Mlaliki 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti nzeru zimateteza+ monga mmene ndalama zimatetezera,+ koma ubwino wa kudziwa zinthu ndi wakuti nzeru zimasunga moyo wa eni nzeruzo.+

  • Mlaliki 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndani angafanane ndi munthu wanzeru?+ Ndipo ndani amadziwa kumasulira zinthu?+ Nzeru za munthu zimachititsa nkhope yake kuwala ndipo ngakhale nkhope yake yokwiya imasintha n’kumaoneka bwino.+

  • Akolose 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chuma chonse chokhudzana ndi nzeru ndiponso kudziwa zinthu+ chinabisidwa mosamala mwa iye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena