Miyambo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+ Miyambo 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anzeru adzapeza ulemu,+ koma opusa amatama zinthu zimene zidzawachititse manyazi.+ Miyambo 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Milomo ya anzeru imafalitsa zimene ikudziwa,+ koma mtima wa anthu opusa suchita zimenezo.+ Miyambo 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Munthu amene khutu lake limamvetsera chidzudzulo+ chopatsa moyo, amakhala pakati pa anthu anzeru.+
5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+
31 Munthu amene khutu lake limamvetsera chidzudzulo+ chopatsa moyo, amakhala pakati pa anthu anzeru.+