Miyambo 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndili ndi malangizo+ ndi nzeru zopindulitsa.+ Ndimamvetsa zinthu,+ ndiponso ndili ndi mphamvu.+ Miyambo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mtima womvetsa ndi umene umafunafuna kudziwa zinthu,+ koma pakamwa pa anthu opusa m’pamene pamafunafuna kulankhula zopusa.+ Mateyu 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mbewu zimene zafesedwa panthaka yabwino, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuzindikira tanthauzo lake, amene amabaladi zipatso. Uyu zipatso 100, uyo 60, winayo 30.”+ Aheberi 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+
14 Ine ndili ndi malangizo+ ndi nzeru zopindulitsa.+ Ndimamvetsa zinthu,+ ndiponso ndili ndi mphamvu.+
14 Mtima womvetsa ndi umene umafunafuna kudziwa zinthu,+ koma pakamwa pa anthu opusa m’pamene pamafunafuna kulankhula zopusa.+
23 Mbewu zimene zafesedwa panthaka yabwino, ndi munthu amene wamva mawu ndi kuzindikira tanthauzo lake, amene amabaladi zipatso. Uyu zipatso 100, uyo 60, winayo 30.”+
14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+