Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 35:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndipo anam’patsa mzimu wa Mulungu kuti akhale wanzeru, wozindikira, wodziwa zinthu, ndi kuti akhale mmisiri waluso pa ntchito ina iliyonse.

  • 1 Mafumu 4:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mulungu anapitiriza kupatsa Solomo nzeru zopanda malire ndi luso lomvetsa zinthu losaneneka.+ Anam’patsanso mtima wozindikira zinthu mwakuya.+

  • 1 Mafumu 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mayi ake anali mkazi wamasiye wa fuko la Nafitali. Bambo ake anali a ku Turo+ odziwa kupanga zinthu ndi mkuwa.+ Hiramu anali wanzeru, womvetsa bwino zinthu,+ ndiponso wodziwa bwino kupanga zinthu zosiyanasiyana zamkuwa. Iye anabwera kwa Mfumu Solomo n’kuyamba kumugwirira ntchito yake yonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena