Miyambo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a anthu oipa amadikirira kukhetsa magazi,+ koma pakamwa pa anthu owongoka mtima m’pamene padzawapulumutse.+ Aroma 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu amakhala ndi chikhulupiriro mumtima mwake+ kuti akhale wolungama, koma ndi pakamwa pake amalengeza poyera+ chikhulupiriro chake kuti apulumuke.
6 Mawu a anthu oipa amadikirira kukhetsa magazi,+ koma pakamwa pa anthu owongoka mtima m’pamene padzawapulumutse.+
10 Munthu amakhala ndi chikhulupiriro mumtima mwake+ kuti akhale wolungama, koma ndi pakamwa pake amalengeza poyera+ chikhulupiriro chake kuti apulumuke.