Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Pitani mukasonkhanitse Ayuda onse amene angapezeke ku Susani+ ndipo musale kudya+ m’malo mwa ine. Musadye kapena kumwa kwa masiku atatu,+ usana ndi usiku. Inenso pamodzi ndi atsikana anga onditumikira+ tisala kudya. Pamenepo, ngakhale kuti ndi zosemphana ndi lamulo, ndidzapita kwa mfumu, ndipo ngati n’kufa,+ ndife.”

  • Esitere 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti ine ndi anthu a mtundu wanga tagulitsidwa+ kuti tiwonongedwe, tiphedwe ndi kufafanizidwa.+ Ngati tikanagulitsidwa kukhala akapolo aamuna+ ndi akapolo aakazi ndikanakhala chete. Koma musalole kuti tsoka limeneli lichitike chifukwa liwonongetsa zinthu zambiri za mfumu.”

  • Miyambo 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chikwapu cha kudzikuza chili m’kamwa mwa wopusa,+ koma anthu anzeru milomo yawo imawatsogolera.+

  • Miyambo 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+ koma pakamwa pa zitsiru pamasefukira mawu opusa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena