Mlaliki 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aliyense wanzeru maso ake amaona bwino,+ koma wopusa amangoyendabe mu mdima waukulu.+ Ineyo ndazindikira kuti onsewa mapeto awo ndi amodzi.+
14 Aliyense wanzeru maso ake amaona bwino,+ koma wopusa amangoyendabe mu mdima waukulu.+ Ineyo ndazindikira kuti onsewa mapeto awo ndi amodzi.+