Miyambo 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nzeru zimakhala pamaso pa munthu womvetsa zinthu,+ koma maso a munthu wopusa ali kumalekezero a dziko lapansi.+ Yohane 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa. 1 Yohane 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma amene amadana ndi m’bale wake ndiye kuti ali mu mdima ndipo akuyenda mu mdimawo,+ ndiponso sakudziwa kumene akupita+ chifukwa maso ake achita khungu chifukwa cha mdimawo.
24 Nzeru zimakhala pamaso pa munthu womvetsa zinthu,+ koma maso a munthu wopusa ali kumalekezero a dziko lapansi.+
19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa.
11 Koma amene amadana ndi m’bale wake ndiye kuti ali mu mdima ndipo akuyenda mu mdimawo,+ ndiponso sakudziwa kumene akupita+ chifukwa maso ake achita khungu chifukwa cha mdimawo.