Mlaliki 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aliyense wanzeru maso ake amaona bwino,+ koma wopusa amangoyendabe mu mdima waukulu.+ Ineyo ndazindikira kuti onsewa mapeto awo ndi amodzi.+ Mlaliki 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndani angafanane ndi munthu wanzeru?+ Ndipo ndani amadziwa kumasulira zinthu?+ Nzeru za munthu zimachititsa nkhope yake kuwala ndipo ngakhale nkhope yake yokwiya imasintha n’kumaoneka bwino.+
14 Aliyense wanzeru maso ake amaona bwino,+ koma wopusa amangoyendabe mu mdima waukulu.+ Ineyo ndazindikira kuti onsewa mapeto awo ndi amodzi.+
8 Ndani angafanane ndi munthu wanzeru?+ Ndipo ndani amadziwa kumasulira zinthu?+ Nzeru za munthu zimachititsa nkhope yake kuwala ndipo ngakhale nkhope yake yokwiya imasintha n’kumaoneka bwino.+