Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+

  • Yobu 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,+

      Amakhala ndi moyo waufupi,+ wodzaza ndi masautso.+

  • Salimo 49:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu, ngakhale atakhala wolemekezeka, koma ngati ali wosazindikira,+

      Amangofanana ndi nyama zimene zaphedwa.+

  • Salimo 73:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+

      Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+

  • 2 Petulo 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena