Miyambo 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Woipa amatenga chiphuphu mobisa,+ kuti akhotetse njira za chiweruzo.+ Miyambo 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa angamwe n’kuiwala malamulo ndi kupondereza ufulu wa ana ovutika.+ Mlaliki 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndaonanso padziko lapansi pano kuti pamene panayenera kukhala chilungamo panali zoipa, ndipo pamene panayenera kuchitika zachilungamo panachitika zoipa.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.
16 Ine ndaonanso padziko lapansi pano kuti pamene panayenera kukhala chilungamo panali zoipa, ndipo pamene panayenera kuchitika zachilungamo panachitika zoipa.+
4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.