Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 21:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno mupeze anthu awiri+ opanda pake+ adzakhale patsogolo pake ndi kupereka umboni wotsutsana naye.+ Adzanene kuti, ‘Iwe watemberera Mulungu ndi mfumu!’+ Kenako mukamutulutse kunja ndi kum’ponya miyala kuti afe.”+

  • Salimo 82:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 “Kodi mudzaweruza mopanda chilungamo,+

      Ndi kukondera anthu oipa kufikira liti?+ [Seʹlah.]

  • Salimo 94:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iwo amaukira koopsa munthu wolungama,+

      Ndipo munthu wosalakwa amamuweruza kuti ndi woipa. Amachita zimenezi kuti akhetse magazi ake.+

  • Yesaya 59:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chilungamo tinachikankhira m’mbuyo,+ ndipo chilungamocho chinakangoima patali.+ Pakuti choonadi chapunthwa ngakhale m’bwalo la mumzinda, ndipo zinthu zolungama zikulephera kulowamo.+

  • Mika 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita bwino kwambiri.+ Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso, ndipo woweruza amalandira chiphuphu poweruza.+ Munthu wotchuka amangolankhula zolakalaka za mtima wake+ ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.

  • Mateyu 26:59
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Pa nthawiyi ansembe aakulu ndi Khoti lonse Lalikulu la Ayuda* anali kufunafuna umboni wonama kuti amunamizire mlandu Yesu ndi kumupha+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena