-
Yobu 33:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ngati iye ali ndi mthenga,
Womulankhulira mmodzi pa omulankhulira 1,000,
Kuti auze munthu zimene zili zowongoka,
-
2 Petulo 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Munthu wolungama ameneyo anali kuzunzika tsiku ndi tsiku ndi zimene anali kuona ndi kumva pamene anali kukhala pakati pawo, ndiponso chifukwa cha zochita zawo zosamvera malamulo.
-
-
-