Miyambo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi munthu wapeza mkazi wabwino?+ Ndiye kuti wapeza chinthu chabwino,+ ndipo Yehova amakondwera naye.+ Miyambo 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkazi wabwino, ndani angam’peze?+ Mtengo wake umaposa wa miyala yamtengo wapatali.
22 Kodi munthu wapeza mkazi wabwino?+ Ndiye kuti wapeza chinthu chabwino,+ ndipo Yehova amakondwera naye.+