Mlaliki 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kwa munthu, palibe chabwino kuposa kuti adye, amwe, ndi kusangalatsa mtima wake chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Ineyo ndaona kuti zimenezinso n’zochokera m’dzanja la Mulungu woona.+ 1 Timoteyo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+
24 Kwa munthu, palibe chabwino kuposa kuti adye, amwe, ndi kusangalatsa mtima wake chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Ineyo ndaona kuti zimenezinso n’zochokera m’dzanja la Mulungu woona.+
17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+