Miyambo 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mumtima mwa munthu womvetsa zinthu mumakhala nzeru,+ ndipo zimadziwika pakati pa anthu opusa. Miyambo 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+ Mlaliki 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+
17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+
25 Ineyo ndinaganiziranso mumtima mwanga+ kuti ndidziwe, ndifufuze, ndiponso ndifunefune nzeru.+ Ndinafunanso kudziwa zimene zimayambitsa zinthu,+ ndiponso kudziwa kuipa kwa kupusa ndi uchitsiru wa misala.+