Yobu 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti inu mukupitiriza kundilembera zinthu zowawa,+Ndipo mukundipatsa zotsatira za zolakwa zimene ndinachita ndili mnyamata.+ Salimo 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+
26 Pakuti inu mukupitiriza kundilembera zinthu zowawa,+Ndipo mukundipatsa zotsatira za zolakwa zimene ndinachita ndili mnyamata.+
7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+