Mlaliki 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi munthu amapeza phindu lanji pa ntchito yake yonse yovuta, imene amaigwira+ mwakhama padziko lapansi pano?*+ Mlaliki 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndinadana ndi moyo+ chifukwa ndinaona kuti ntchito imene yachitidwa padziko lapansi pano ndi yosautsa mtima.+ Pakuti zonse zinali zachabechabe ndipo kuchita zimenezi kunali ngati kuthamangitsa mphepo.+ Mateyu 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi munthu angapindulenji ngati atapeza zinthu zonse za m’dzikoli koma n’kutaya moyo wake?+ Kapena munthu angapereke chiyani chosinthanitsa+ ndi moyo wake? 1 Timoteyo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti sitinabwere ndi kanthu m’dziko, ndipo sitingatulukemo ndi kanthu.+
3 Kodi munthu amapeza phindu lanji pa ntchito yake yonse yovuta, imene amaigwira+ mwakhama padziko lapansi pano?*+
17 Ine ndinadana ndi moyo+ chifukwa ndinaona kuti ntchito imene yachitidwa padziko lapansi pano ndi yosautsa mtima.+ Pakuti zonse zinali zachabechabe ndipo kuchita zimenezi kunali ngati kuthamangitsa mphepo.+
26 Kodi munthu angapindulenji ngati atapeza zinthu zonse za m’dzikoli koma n’kutaya moyo wake?+ Kapena munthu angapereke chiyani chosinthanitsa+ ndi moyo wake?