Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho ndinaona ntchito zonse zimene zinachitidwa padziko lapansi pano,+ ndipo ndinapeza kuti zonse ndi zachabechabe ndiponso zili ngati kuthamangitsa mphepo.+

  • Mlaliki 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti pali munthu amene ntchito yake yovuta waigwira mwanzeru, mozindikira ndiponso waigwira bwino.+ Koma zonse zimene anapeza zidzaperekedwa kwa munthu amene sanagwire mwakhama ntchito ngati imeneyo.+ Zimenezinso n’zachabechabe ndipo n’zomvetsa chisoni kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena