Genesis 31:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndinkangokhalira kutenthedwa ndi dzuwa usana ndi kuzizidwa ndi mphepo usiku, ndipo tulo sindinkationa.+ Danieli 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako mfumu inapita kunyumba yake yachifumu. Usiku umenewo mfumuyo inasala kudya+ ndipo sanaiimbire nyimbo ndi zipangizo zoimbira, komanso sinathe kugona tulo.+ Luka 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho lekani kudera nkhawa za chimene mudzadya ndi chimene mudzamwa, ndipo siyani kuvutika mumtima.+
40 Ndinkangokhalira kutenthedwa ndi dzuwa usana ndi kuzizidwa ndi mphepo usiku, ndipo tulo sindinkationa.+
18 Kenako mfumu inapita kunyumba yake yachifumu. Usiku umenewo mfumuyo inasala kudya+ ndipo sanaiimbire nyimbo ndi zipangizo zoimbira, komanso sinathe kugona tulo.+
29 Choncho lekani kudera nkhawa za chimene mudzadya ndi chimene mudzamwa, ndipo siyani kuvutika mumtima.+