Esitere 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usiku umenewo mfumu inasowa tulo.+ Choncho inaitanitsa buku limene anali kulembamo zochitika+ za m’masiku amenewo. Ndiyeno anawerenga zochitikazo pamaso pa mfumu. Danieli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’chaka chachiwiri cha ufumu wa Nebukadinezara, Nebukadinezarayo analota maloto.+ Malotowo anamuvutitsa maganizo+ ndipo tulo tinamuthera.
6 Usiku umenewo mfumu inasowa tulo.+ Choncho inaitanitsa buku limene anali kulembamo zochitika+ za m’masiku amenewo. Ndiyeno anawerenga zochitikazo pamaso pa mfumu.
2 M’chaka chachiwiri cha ufumu wa Nebukadinezara, Nebukadinezarayo analota maloto.+ Malotowo anamuvutitsa maganizo+ ndipo tulo tinamuthera.