Miyambo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi m’dzanja la Yehova.+ Amautembenuzira kulikonse kumene iye akufuna.+ Danieli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’chaka chachiwiri cha ufumu wa Nebukadinezara, Nebukadinezarayo analota maloto.+ Malotowo anamuvutitsa maganizo+ ndipo tulo tinamuthera. Danieli 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako mfumu inapita kunyumba yake yachifumu. Usiku umenewo mfumuyo inasala kudya+ ndipo sanaiimbire nyimbo ndi zipangizo zoimbira, komanso sinathe kugona tulo.+
21 Mtima wa mfumu uli ngati mitsinje yamadzi m’dzanja la Yehova.+ Amautembenuzira kulikonse kumene iye akufuna.+
2 M’chaka chachiwiri cha ufumu wa Nebukadinezara, Nebukadinezarayo analota maloto.+ Malotowo anamuvutitsa maganizo+ ndipo tulo tinamuthera.
18 Kenako mfumu inapita kunyumba yake yachifumu. Usiku umenewo mfumuyo inasala kudya+ ndipo sanaiimbire nyimbo ndi zipangizo zoimbira, komanso sinathe kugona tulo.+