2 Samueli 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero Davide anayamba kuchonderera Mulungu woona chifukwa cha mwanayo, ndipo anasiyiratu kudya.+ Kenako Davide analowa m’nyumba ndipo usiku umenewo anagona pansi.+ 1 Mafumu 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+
16 Zitatero Davide anayamba kuchonderera Mulungu woona chifukwa cha mwanayo, ndipo anasiyiratu kudya.+ Kenako Davide analowa m’nyumba ndipo usiku umenewo anagona pansi.+
27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+