Yesaya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’tsiku limenelo, Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri+ kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,+ ku Hamati ndi m’zilumba za m’nyanja.+ Yesaya 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero pakatikati pa dzikolo, pakati pa anthu a mitundu ina, anthu anga adzakhala ngati zipatso zotsala mumtengo wa maolivi,+ ndiponso ngati zokunkha zotsala anthu akakolola mphesa.+
11 M’tsiku limenelo, Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri+ kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,+ ku Hamati ndi m’zilumba za m’nyanja.+
13 Chotero pakatikati pa dzikolo, pakati pa anthu a mitundu ina, anthu anga adzakhala ngati zipatso zotsala mumtengo wa maolivi,+ ndiponso ngati zokunkha zotsala anthu akakolola mphesa.+