Yesaya 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Babulo, amene ndi chokongoletsera maufumu,+ chinthu chokongola ndi chonyadira cha Akasidi,+ adzakhala ngati pamene Mulungu anagonjetsa Sodomu ndi Gomora.+ Yesaya 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Ine ndidzawaukira,”+ watero Yehova wa makamu. “M’Babulo ndidzachotsamo dzina,+ anthu otsala, ana, ndi mbadwa,”+ watero Yehova. Yesaya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano taonani! Kukubwera magaleta ankhondo okokedwa ndi mahatchi awiriawiri, mutakwera amuna ankhondo.”+ Kenako iye anayamba kufuula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+
19 Babulo, amene ndi chokongoletsera maufumu,+ chinthu chokongola ndi chonyadira cha Akasidi,+ adzakhala ngati pamene Mulungu anagonjetsa Sodomu ndi Gomora.+
22 “Ine ndidzawaukira,”+ watero Yehova wa makamu. “M’Babulo ndidzachotsamo dzina,+ anthu otsala, ana, ndi mbadwa,”+ watero Yehova.
9 Tsopano taonani! Kukubwera magaleta ankhondo okokedwa ndi mahatchi awiriawiri, mutakwera amuna ankhondo.”+ Kenako iye anayamba kufuula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+